Ekisodo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Mose anachonderera Yehova Mulungu wake+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani inu Yehova mukufuna kuti mkwiyo wanu uyakire anthu anu, pambuyo powatulutsa mʼdziko la Iguputo pogwiritsa ntchito mphamvu zazikulu ndiponso dzanja lamphamvu?+
11 Kenako Mose anachonderera Yehova Mulungu wake+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani inu Yehova mukufuna kuti mkwiyo wanu uyakire anthu anu, pambuyo powatulutsa mʼdziko la Iguputo pogwiritsa ntchito mphamvu zazikulu ndiponso dzanja lamphamvu?+