Deuteronomo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kwera pamwamba pa Pisiga+ ndipo ukayangʼane kumadzulo, kumpoto, kumʼmwera ndi kumʼmawa kuti ukaone dzikolo ndi maso ako, chifukwa suwoloka Yorodano uyu.+ Deuteronomo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Mose anachoka mʼchipululu cha Mowabu kupita mʼphiri la Nebo,+ pamwamba pa Pisiga,+ moyangʼanizana ndi Yeriko.+ Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse, kuchokera ku Giliyadi mpaka ku Dani.+
27 Kwera pamwamba pa Pisiga+ ndipo ukayangʼane kumadzulo, kumpoto, kumʼmwera ndi kumʼmawa kuti ukaone dzikolo ndi maso ako, chifukwa suwoloka Yorodano uyu.+
34 Kenako Mose anachoka mʼchipululu cha Mowabu kupita mʼphiri la Nebo,+ pamwamba pa Pisiga,+ moyangʼanizana ndi Yeriko.+ Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse, kuchokera ku Giliyadi mpaka ku Dani.+