Numeri 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Balaki anatenga Balamu nʼkupita naye pamwamba pa phiri la Peori, limene linayangʼanizana ndi Yesimoni.*+
28 Choncho Balaki anatenga Balamu nʼkupita naye pamwamba pa phiri la Peori, limene linayangʼanizana ndi Yesimoni.*+