Salimo 135:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anawononga mitundu yambiri+Ndipo anapha mafumu amphamvu+11 Anapha Sihoni mfumu ya Aamori,+Ogi mfumu ya Basana+Komanso anawononga maufumu onse a ku Kanani.
10 Anawononga mitundu yambiri+Ndipo anapha mafumu amphamvu+11 Anapha Sihoni mfumu ya Aamori,+Ogi mfumu ya Basana+Komanso anawononga maufumu onse a ku Kanani.