33 Choncho Mose anapereka malo kwa ana a Gadi, ana a Rubeni+ komanso hafu ya fuko la Manase+ mwana wa Yosefe. Anawapatsa malo a ufumu wa Sihoni+ mfumu ya Aamori, malo a ufumu wa Ogi+ mfumu ya Basana ndi dera lonse la mizinda komanso midzi yozungulira.