Numeri 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anali ndi ziweto zambiri ndipo anaona kuti dera la Yazeri+ komanso la Giliyadi, anali malo abwino a ziweto. 1 Mbiri 6:77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa anthu a ku banja la Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto. 1 Mbiri 6:81 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 mzinda wa Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto.
32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anali ndi ziweto zambiri ndipo anaona kuti dera la Yazeri+ komanso la Giliyadi, anali malo abwino a ziweto.
77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa anthu a ku banja la Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.
81 mzinda wa Hesiboni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Yazeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto.