-
Deuteronomo 20:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Iye aziwauza kuti, ‘Tamverani Aisiraeli inu. Mwatsala pangʼono kumenyana ndi adani anu. Mitima yanu isachite mantha. Musaope, kuchita mantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,
-