-
Deuteronomo 3:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno Yehova anandiuza kuti, ‘Usamuope ameneyu, chifukwa ndipereka iyeyo pamodzi ndi anthu ake onse komanso dziko lake mʼmanja mwako. Umuchite zimene unachitira Sihoni mfumu ya Aamori, amene ankakhala ku Hesiboni.’
-