Salimo 89:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndalumbira kamodzi kokha pa kuyera kwanga.Davide sindidzamunamiza.+ Tito 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zinthu zimenezi timakhala nazo chifukwa cha chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chimene Mulungu amene sanganame+ analonjeza kalekale.
2 Zinthu zimenezi timakhala nazo chifukwa cha chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chimene Mulungu amene sanganame+ analonjeza kalekale.