2 Samueli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndipo anawagoneka pansi nʼkuyamba kuwayeza ndi chingwe. Ankati akayeza zingwe ziwiri, anthu amenewo ankawapha ndipo akayeza chingwe chimodzi, amenewo ankawasiya ndi moyo.+ Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo ankapereka msonkho kwa iye.+ 1 Mbiri 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagonjetsa Amowabu+ moti Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo ankapereka msonkho kwa iye.+ Salimo 108:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+ Edomu ndidzamuponyera nsapato zanga.+ Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+
2 Davide anagonjetsanso Amowabu+ ndipo anawagoneka pansi nʼkuyamba kuwayeza ndi chingwe. Ankati akayeza zingwe ziwiri, anthu amenewo ankawapha ndipo akayeza chingwe chimodzi, amenewo ankawasiya ndi moyo.+ Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo ankapereka msonkho kwa iye.+
2 Kenako anagonjetsa Amowabu+ moti Amowabuwo anakhala atumiki a Davide ndipo ankapereka msonkho kwa iye.+
9 Mowabu ndi beseni langa losambiramo.+ Edomu ndidzamuponyera nsapato zanga.+ Ndidzafuula mosangalala chifukwa chogonjetsa Filisitiya.”+