Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 27:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma Isaki anayankha Esau kuti: “Taona, iye uja ndamuika kukhala mbuye wako.+ Ndamupatsa abale ake onse kuti akhale atumiki ake. Komanso ndamudalitsa kuti akhale ndi zokolola zambiri ndiponso vinyo watsopano wambiri.+ Nanga chatsalanso nʼchiyani choti ndikuchitire mwana wanga?”

  • 2 Samueli 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Davide anakhazikitsa midzi ya asilikali ku Edomu. Mu Edomu monse anaikamo midzi ya asilikali, moti Aedomu anakhala antchito a Davide+ ndipo Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+

  • Amosi 9:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ‘Pa tsiku limenelo, ndidzadzutsa nyumba* ya Davide+ imene inagwa,

      Ndi kukonza malo amene khoma lake linawonongeka.

      Ndidzaikonza kuti isakhalenso bwinja.

      Ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati mmene inalili kale.+

      12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga atenge zinthu zotsala za Edomu.+

      Ndiponso za mitundu yonse ya anthu imene inkaitanira pa dzina langa,’ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena