Genesis 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Esau anakakhazikika kudera lamapiri ku Seiri.+ Dzina lina la Esau linali Edomu.+ Yoswa 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo Isaki ndinamʼpatsa Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinamʼpatsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+
4 ndipo Isaki ndinamʼpatsa Yakobo ndi Esau.+ Pambuyo pake Esau ndinamʼpatsa phiri la Seiri kuti likhale lake.+ Kenako Yakobo ndi ana ake anapita ku Iguputo.+