Ekisodo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamaleki+ anabwera kudzamenyana ndi Isiraeli ku Refidimu.+ Ekisodo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi mʼbuku kuti anthu azidzazikumbukira ndipo umuuze Yoswa kuti, ‘Ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi ndipo sadzakumbukiridwa nʼkomwe.’”+
14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi mʼbuku kuti anthu azidzazikumbukira ndipo umuuze Yoswa kuti, ‘Ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi ndipo sadzakumbukiridwa nʼkomwe.’”+