Ekisodo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Samalani kuti musachite pangano ndi anthu okhala mʼdzikomo, chifukwa akamachita uhule ndi milungu yawo komanso kupereka nsembe kwa milungu yawo,+ wina adzakuitanani kunyumba kwake ndipo nanunso mudzadya nsembe yakeyo.+ 1 Akorinto 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ayi, koma ndikutanthauza kuti zinthu zimene anthu a mitundu ina amapereka nsembe amazipereka kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+ Ndipo sindikufuna kuti muzichita chilichonse chogwirizana ndi ziwanda.+
15 Samalani kuti musachite pangano ndi anthu okhala mʼdzikomo, chifukwa akamachita uhule ndi milungu yawo komanso kupereka nsembe kwa milungu yawo,+ wina adzakuitanani kunyumba kwake ndipo nanunso mudzadya nsembe yakeyo.+
20 Ayi, koma ndikutanthauza kuti zinthu zimene anthu a mitundu ina amapereka nsembe amazipereka kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+ Ndipo sindikufuna kuti muzichita chilichonse chogwirizana ndi ziwanda.+