Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori. Yehova Mulungu wanu anawononga pakati panu munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori.+

  • Yoswa 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kodi zoipa zimene tinachita ku Peori zatichepera? Sitinadziyeretsebe ku tchimo limene lija mpaka lero, ngakhale kuti mliri unagwera anthu a Yehova.+

  • Salimo 106:28, 29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kenako iwo anayamba kulambira* Baala wa ku Peori,+

      Ndipo anadya nsembe zoperekedwa kwa akufa.*

      29 Iwo anamukwiyitsa chifukwa cha zochita zawo,+

      Ndipo pakati pawo panagwa mliri.+

  • Hoseya 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Isiraeli ndinamupeza ali ngati mphesa zamʼchipululu.+

      Ndinaona makolo anu ali ngati nkhuyu zoyambirira pamtengo wa mkuyu.

      Koma anapita kwa Baala wa ku Peori,+

      Anadzipereka kwa chinthu chochititsa manyazichi.*+

      Ndipo anakhala onyansa ngati chinthu chimene ankachikondacho.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena