Yoswa 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha Aisiraeli. Palibe amene ankatuluka kapena kulowa mumzindawo.+
6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha Aisiraeli. Palibe amene ankatuluka kapena kulowa mumzindawo.+