Genesis 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Leya anakhala woyembekezera ndipo anabereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Rubeni,*+ ndipo anati: “Chifukwa Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda.”
32 Choncho Leya anakhala woyembekezera ndipo anabereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Rubeni,*+ ndipo anati: “Chifukwa Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda.”