Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mose anauza Kora ndi anthu onse amene ankamutsatira kuti: “Mawa mʼmamawa, Yehova adzasonyeza munthu amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera, amene ali woyenera kuyandikira pamaso pake.+ Ndipo amene ati adzamusankheyo+ adzayandikira pamaso pake.

  • Numeri 16:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kora atasonkhanitsa anthu onse omutsatira+ kuti atsutsane nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera ku gulu lonselo.+

  • Deuteronomo 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 kapena zimene anachitira Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, mwana wa Rubeni, pamene dziko linatsegula pakamwa pake nʼkuwameza pamodzi ndi mabanja awo, matenti awo ndi chamoyo chilichonse chimene anali nacho. Dziko linawameza Aisiraeli onse akuona.+

  • Salimo 106:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako dziko lapansi linatseguka ndipo linameza Datani,

      Nʼkukwirira anthu onse amene anali kumbali ya Abiramu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena