Numeri 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthakayo inangʼambika* nʼkuwameza limodzi ndi mabanja awo komanso anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora+ pamodzi ndi katundu wawo yense. Numeri 16:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako moto unachokera kwa Yehova+ ndipo unapsereza amuna 250 omwe ankapereka nsembe zofukiza aja.+ Salimo 106:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Moto unayaka pakati pa gulu lawo.Malawi amoto anapsereza oipa.+
32 Nthakayo inangʼambika* nʼkuwameza limodzi ndi mabanja awo komanso anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora+ pamodzi ndi katundu wawo yense.
35 Kenako moto unachokera kwa Yehova+ ndipo unapsereza amuna 250 omwe ankapereka nsembe zofukiza aja.+