Genesis 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko Yuda anaona mwana wamkazi wa munthu wina wa Chikanani+ ndipo anamukwatira. Munthuyo dzina lake anali Sua. Genesis 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaberekanso mwana wina wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Shela. Pa nthawi imene mwanayu ankabadwa, Yuda anali ku Akizibu.+ Genesis 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Yuda atayangʼanitsitsa zinthuzo, ananena kuti: “Mkaziyu ndi wolungama koposa ine, chifukwa sindinamupereke kwa mwana wanga Shela.”+ Zitatero, Yuda sanagonenso naye. 1 Mbiri 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana a Shela+ mwana wa Yuda anali Ere bambo a Leka, Laada bambo a Maresha, mabanja a Asibeya omwe ankagwira ntchito yopanga nsalu zabwino kwambiri,
2 Kumeneko Yuda anaona mwana wamkazi wa munthu wina wa Chikanani+ ndipo anamukwatira. Munthuyo dzina lake anali Sua.
5 Anaberekanso mwana wina wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Shela. Pa nthawi imene mwanayu ankabadwa, Yuda anali ku Akizibu.+
26 Ndiyeno Yuda atayangʼanitsitsa zinthuzo, ananena kuti: “Mkaziyu ndi wolungama koposa ine, chifukwa sindinamupereke kwa mwana wanga Shela.”+ Zitatero, Yuda sanagonenso naye.
21 Ana a Shela+ mwana wa Yuda anali Ere bambo a Leka, Laada bambo a Maresha, mabanja a Asibeya omwe ankagwira ntchito yopanga nsalu zabwino kwambiri,