Nehemiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mukadzabwerera kwa ine nʼkumatsatira malamulo anga, ngakhale anthu a mtundu wanu atamwazikira kumalekezero akumwamba, ndidzawasonkhanitsa+ kuchokera kumeneko nʼkuwabweretsa kumalo amene ndasankha kuti kukhale dzina langa.’+ Machitidwe 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa zibwere kuchokera kwa Yehova.*
9 Koma mukadzabwerera kwa ine nʼkumatsatira malamulo anga, ngakhale anthu a mtundu wanu atamwazikira kumalekezero akumwamba, ndidzawasonkhanitsa+ kuchokera kumeneko nʼkuwabweretsa kumalo amene ndasankha kuti kukhale dzina langa.’+
19 Choncho lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa zibwere kuchokera kwa Yehova.*