Yesaya 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine sindinalankhule mʼmalo obisika,+ mʼdziko lamdima.Sindinauze mbadwa* za Yakobo kuti,‘Muzindifunafuna pachabe.’ Ine ndine Yehova, amene ndimalankhula zolungama komanso kulengeza zinthu zimene ndi zolondola.+
19 Ine sindinalankhule mʼmalo obisika,+ mʼdziko lamdima.Sindinauze mbadwa* za Yakobo kuti,‘Muzindifunafuna pachabe.’ Ine ndine Yehova, amene ndimalankhula zolungama komanso kulengeza zinthu zimene ndi zolondola.+