Aroma 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma kodi lemba limati chiyani? Limati: “Mawu a chilamulowo ali pafupi ndi inu, ali mʼkamwa mwanu ndi mumtima mwanu,”+ amenewa ndi “mawu” a chikhulupiriro amene tikulalikira.
8 Koma kodi lemba limati chiyani? Limati: “Mawu a chilamulowo ali pafupi ndi inu, ali mʼkamwa mwanu ndi mumtima mwanu,”+ amenewa ndi “mawu” a chikhulupiriro amene tikulalikira.