Deuteronomo 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onani, lero ndikuika dalitso ndi temberero pamaso panu:+ Deuteronomo 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a mʼChilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’”) Deuteronomo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mudzalandira madalitso onsewa ndipo zinthu zabwino zonsezi zidzakhala zanu,+ mukapitiriza kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu: Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
26 ‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a mʼChilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’”)
2 Mudzalandira madalitso onsewa ndipo zinthu zabwino zonsezi zidzakhala zanu,+ mukapitiriza kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu:
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+