Salimo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye amakonda chilungamo ndipo amaweruza mosakondera.+ Dziko lapansi ladzaza ndi chikondi chokhulupirika cha Yehova.+
5 Iye amakonda chilungamo ndipo amaweruza mosakondera.+ Dziko lapansi ladzaza ndi chikondi chokhulupirika cha Yehova.+