Deuteronomo 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga! Oweruza 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma woweruza akamwalira, iwo ankayambiranso kuchita zoipa kuposa makolo awo. Ankatsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Iwo sanasiye zochita zawozo ndiponso unkhutukumve wawo. Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+
27 Ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma mtima* kwanu.+ Ngati mwakhala mukupandukira Yehova pamene ndili moyo, ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!
19 Koma woweruza akamwalira, iwo ankayambiranso kuchita zoipa kuposa makolo awo. Ankatsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Iwo sanasiye zochita zawozo ndiponso unkhutukumve wawo.
14 Munthu wopusa* amanena mumtima mwake kuti: “Kulibe Yehova.”+ Zochita za anthu amenewa ndi zoipa komanso zonyansa,Ndipo palibe amene akuchita zabwino.+