-
Genesis 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mwa anthu amenewa, munachokera anthu okhala mʼzilumba amene anafalikira mʼzilumbazo malinga ndi zilankhulo zawo, mabanja awo ndi mitundu yawo.
-