Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya. Hoseya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe unakhuta chifukwa unali ndi zakudya zambiri.+Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kunyada. Choncho unandiiwala.+
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya.
6 Iwe unakhuta chifukwa unali ndi zakudya zambiri.+Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kunyada. Choncho unandiiwala.+