1 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho analirira Yehova kuti awathandize+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ chifukwa tasiya Yehova nʼkuyamba kutumikira Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tipulumutseni kwa adani athu kuti tizikutumikirani.’ 1 Samueli 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musapatuke nʼkuyamba kutsatira milungu yopanda pake*+ yomwe ndi yosathandiza+ komanso singakupulumutseni chifukwa ndi yopanda pake.*
10 Choncho analirira Yehova kuti awathandize+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ chifukwa tasiya Yehova nʼkuyamba kutumikira Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tipulumutseni kwa adani athu kuti tizikutumikirani.’
21 Musapatuke nʼkuyamba kutsatira milungu yopanda pake*+ yomwe ndi yosathandiza+ komanso singakupulumutseni chifukwa ndi yopanda pake.*