Aroma 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso ndifunse kuti, Kodi si zoona kuti Aisiraeli anadziwa?+ Choyamba Mose anati: “Ndidzakuchititsani nsanje pogwiritsa ntchito anthu omwe si Aisiraeli. Ndidzakukwiyitsani koopsa pogwiritsa ntchito mtundu wopusa.”+
19 Komanso ndifunse kuti, Kodi si zoona kuti Aisiraeli anadziwa?+ Choyamba Mose anati: “Ndidzakuchititsani nsanje pogwiritsa ntchito anthu omwe si Aisiraeli. Ndidzakukwiyitsani koopsa pogwiritsa ntchito mtundu wopusa.”+