Maliro 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani, inu Yehova. Ine ndili pamavuto aakulu. Mʼmimba mwanga mukubwadamuka. Mtima wanga wasweka, chifukwa ndapanduka kwambiri.+ Panja, lupanga lapha ana anga.+ Mʼnyumba, anthu akufanso.
20 Taonani, inu Yehova. Ine ndili pamavuto aakulu. Mʼmimba mwanga mukubwadamuka. Mtima wanga wasweka, chifukwa ndapanduka kwambiri.+ Panja, lupanga lapha ana anga.+ Mʼnyumba, anthu akufanso.