Ezekieli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Lupanga lidzapha anthu amene ali kunja kwa mzinda+ ndipo mliri ndi njala zidzapha amene ali mkati mwa mzinda. Aliyense amene ali kunja kwa mzinda adzaphedwa ndi lupanga ndipo amene ali mumzinda adzafa ndi njala komanso mliri.+
15 Lupanga lidzapha anthu amene ali kunja kwa mzinda+ ndipo mliri ndi njala zidzapha amene ali mkati mwa mzinda. Aliyense amene ali kunja kwa mzinda adzaphedwa ndi lupanga ndipo amene ali mumzinda adzafa ndi njala komanso mliri.+