1 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya anthu ake,+ popeza Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+ Ezekieli 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+
22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya anthu ake,+ popeza Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+
14 Ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.+