Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nahumu 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.

      Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi wokonzeka kusonyeza mkwiyo wake.+

      Yehova amabwezera adani ake,

      Ndipo adani ake amawasungira mkwiyo.

  • Aroma 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Okondedwa, musamabwezere zoipa, koma siyirani malo mkwiyo wa Mulungu.+ Chifukwa Malemba amati: “‘Kubwezera ndi kwanga, ndidzawabwezera ndine,’ watero Yehova.”*+

  • Aheberi 10:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Popeza tikumudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.” Amenenso anati: “Yehova* adzaweruza anthu ake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena