Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Choncho Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,

      Mulungu Wamphamvu wa Isiraeli, wanena kuti:

      “Eya! Ndidzachotsa adani anga pamaso panga,

      Ndipo ndidzabwezera adani anga.+

  • Yesaya 59:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye adzawapatsa mphoto chifukwa cha zimene achita:+

      Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango.+

      Ndipo zilumba adzazipatsa chilango chogwirizana ndi zochita zawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena