-
Deuteronomo 31:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Choncho Mose analemba nyimboyi pa tsiku limenelo nʼkuphunzitsa Aisiraeli.
23 Ndiyeno Mulungu anaika Yoswa+ mwana wa Nuni kuti akhale mtsogoleri, ndipo anamuuza kuti: “Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ chifukwa iwe ndi amene udzalowetse Aisiraeli mʼdziko limene ndawalumbirira,+ ndipo ine ndidzapitiriza kukhala ndi iwe.”
-