-
2 Mbiri 17:8, 9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Anawaitana pamodzi ndi Alevi awa: Semaya, Netaniya, Zebadiya, Asaheli, Semiramoti, Yehonatani, Adoniya, Tobiya ndi Tobi-adoniya, pamodzinso ndi Elisama ndi Yehoramu omwe anali ansembe.+ 9 Iwo anayamba kuphunzitsa mu Yuda ndipo ankatenga buku la Chilamulo cha Yehova.+ Ankayenda mʼmizinda yonse ya Yuda nʼkumaphunzitsa anthu.
-