Levitiko 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Matumbo ake ndi ziboda zake azizitsuka ndi madzi. Akatero wansembe aziwotcha nyama yonse kuti paguwa lansembe pakhale utsi, ndipo ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto, yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.+
9 Matumbo ake ndi ziboda zake azizitsuka ndi madzi. Akatero wansembe aziwotcha nyama yonse kuti paguwa lansembe pakhale utsi, ndipo ikhale nsembe yopsereza. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto, yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.+