Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Dziko limene ndidzakupatsani lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita zimenezi chifukwa anthu okhala mʼdzikomo ndidzawapereka mʼmanja mwanu ndipo inu mudzawathamangitsa pamaso panu.+

  • Numeri 34:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Upereke malangizo awa kwa Aisiraeli: ‘Awa ndi malire a dziko la Kanani, dziko limene ndidzakupatseni kuti likhale cholowa chanu.+

  • Numeri 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Malire anu a mbali yakumadzulo akakhale gombe la Nyanja Yaikulu.* Amenewa akakhale malire anu a mbali yakumadzulo.+

  • Deuteronomo 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Malo alionse amene mapazi anu adzaponde adzakhala anu.+ Malire a dziko lanu adzayambira kuchipululu kukafika ku Lebanoni, kuyambira ku mtsinje wa Firate, kukafika kunyanja yakumadzulo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena