Ekisodo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ ndipo ndidzathamangitsa Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Yoswa 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yoswa anati: “Mukaona zimene zichitike pano, mudziwa kuti Mulungu wamoyo ali pakati panu+ ndipo adzathamangitsadi Akanani, Ahiti, Ahivi, Aperezi, Agirigasi, Aamori ndi Ayebusi.+
2 Ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ ndipo ndidzathamangitsa Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
10 Kenako Yoswa anati: “Mukaona zimene zichitike pano, mudziwa kuti Mulungu wamoyo ali pakati panu+ ndipo adzathamangitsadi Akanani, Ahiti, Ahivi, Aperezi, Agirigasi, Aamori ndi Ayebusi.+