Ekisodo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho uwauze Aisiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndidzakupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani ndipo ndidzakulanditsani kuti musakhalenso akapolo awo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula* komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+ Ekisodo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lalero limene mwatuluka mu Iguputo,+ mʼnyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova wakutulutsani mʼdzikoli ndi dzanja lake lamphamvu.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi zofufumitsa. Ekisodo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno mʼtsogolo ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ mudzawayankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi dzanja lake lamphamvu mu Iguputo, mʼnyumba ya ukapolo.+
6 Choncho uwauze Aisiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndidzakupulumutsani ku ntchito yokakamiza imene Aiguputo akukugwiritsani ndipo ndidzakulanditsani kuti musakhalenso akapolo awo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula* komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+
3 Kenako Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lalero limene mwatuluka mu Iguputo,+ mʼnyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova wakutulutsani mʼdzikoli ndi dzanja lake lamphamvu.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.
14 Ndiyeno mʼtsogolo ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ mudzawayankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi dzanja lake lamphamvu mu Iguputo, mʼnyumba ya ukapolo.+