Deuteronomo 33:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”* Salimo 147:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake. Tamandani Ya!*+
29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”*
20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake. Tamandani Ya!*+