Ekisodo 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mʼdziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku a moyo wanu.* Deuteronomo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzakupatsani ana ambiri komanso ziweto zochuluka ndipo nthaka+ yamʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzakupatsani, idzabereka zipatso zambiri.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndi mphoto yochokera kwa Mulungu.+
26 Mʼdziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku a moyo wanu.*
11 Yehova adzakupatsani ana ambiri komanso ziweto zochuluka ndipo nthaka+ yamʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzakupatsani, idzabereka zipatso zambiri.+
3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndi mphoto yochokera kwa Mulungu.+