Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+ Deuteronomo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova adzakulangani ndi zithupsa za ku Iguputo, matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo simudzachira matenda amenewa.
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
27 Yehova adzakulangani ndi zithupsa za ku Iguputo, matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo simudzachira matenda amenewa.