Numeri 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma amuna amene anapita naye limodzi ananena kuti: “Sitingathe kukalimbana nawo anthuwo, chifukwa ndi amphamvu kuposa ifeyo.”+
31 Koma amuna amene anapita naye limodzi ananena kuti: “Sitingathe kukalimbana nawo anthuwo, chifukwa ndi amphamvu kuposa ifeyo.”+