Ekisodo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Mose anatembenuka nʼkutsika mʼphirimo atanyamula miyala yosema ya Umboni+ mʼmanja mwake.+ Pamiyalayo analembapo mawu mbali zonse ziwiri. Anawalemba kutsogolo ndi kumbuyo kwake.
15 Kenako Mose anatembenuka nʼkutsika mʼphirimo atanyamula miyala yosema ya Umboni+ mʼmanja mwake.+ Pamiyalayo analembapo mawu mbali zonse ziwiri. Anawalemba kutsogolo ndi kumbuyo kwake.