Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Muziyenda mʼnjira imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo, kuti zinthu zikuyendereni bwino komanso kuti mukhale ndi moyo wautali mʼdziko limene mudzalitenge kuti likhale lanu.”+

  • Yoswa 22:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma mukaonetsetse kuti mukutsatira Chilamulo ndiponso malamulo amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani.+ Muzikakonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda mʼnjira zake zonse,+ kumvera malamulo ake,+ kumʼmamatira+ ndiponso kumʼtumikira+ ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena