Salimo 68:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Bambo wa ana amasiye komanso amene amateteza* akazi amasiye+Ndi Mulungu amene amakhala mʼmalo ake oyera.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+
5 Bambo wa ana amasiye komanso amene amateteza* akazi amasiye+Ndi Mulungu amene amakhala mʼmalo ake oyera.+
27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+