17 Simudzaloledwa kudyera mʼmizinda yanu chakhumi cha mbewu zanu, vinyo wanu watsopano, mafuta anu, ana oyamba kubadwa a ngʼombe zanu ndi a nkhosa zanu,+ iliyonse mwa nsembe zimene mukupereka pokwaniritsa lonjezo limene mwachita, nsembe zanu zaufulu kapena chopereka chochokera mʼmanja mwanu.