Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti munthu wachitadi cholakwa kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wochokera kwa* mboni ziwiri kapena zitatu.+ 1 Timoteyo 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usavomereze mlandu woneneza mwamuna wachikulire,* kupatulapo ngati pali mboni ziwiri kapena zitatu.+
15 Mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti munthu wachitadi cholakwa kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wochokera kwa* mboni ziwiri kapena zitatu.+
19 Usavomereze mlandu woneneza mwamuna wachikulire,* kupatulapo ngati pali mboni ziwiri kapena zitatu.+